Ogwira ntchito pa chipatala chaching’ono cha Malomo m’boma la Ntchisi apempha boma kuti liwawonjezere ogwira ntchito pa malowo. Chipatalachi chimafikira anthu opitilira 70,000 ozungulira derali mpaka kufikiranso mbali zina ndipo patsiku amathandiza anthu opitilira 3000. Mmodzi wa mkulu woyang’anira pa chipatalachi a Zuze Khonde anawuza wachiwiri kwa nduna ya zaumoyo a Halima Daudi omwe anayendera […]
The post “Ma dotolo tilipo atatu, anamwino asanu koma patsiku timathandiza odwala kupitilira 3000” appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.
Moni Malawi 
