Lilongwe Water Board (LWB) yati ndiyokhumudwa ndi mchitidwe wa anthu ena omwe amasankha kusanena nsanga za mapaipi amadzi omwe ophulika m’madera momwe akukhala ndicholinga choti azitunga madzi aulele. Izi zikudza pomwe mmadera ena monga Kaliyeka, Kawale, Area 25, Likuni kungotchulapo ochepa, anthu ena amasankha kusanena mwa changu za mapaipi a waterboard omwe aphulika mmadera mwawo. […]
The post LWB yati ndiyokhumudwa ndi mchitidwe wa anthu ena osanena za mapaipi a madzi ophulika appeared first on Malawi24.