Katswiri pa nkhani za malamulo a Stanley Chirwa omwe amayimilira anthu pa milandu, ali m’manja mwa apolisi powaganizira kuti anagula galimoto yomwe inabedwa m’dziko la South Africa ndi zigawenga zokhala ndi mfuti. Ofalitsa nkhani za a Polisi m’dziko muno, a Peter Kalaya, ndi omwe atsimikiza za nkhaniyi ponena kuti a Chirwa amangidwa kumapeto kwa sabata […]
The post Loya wanjatidwa kamba kogula galimoto yobedwa ku South Africa appeared first on Malawi 24.