Bungwe la Church and Society mu mpingo wa CCAP mu Synod ya Livingstonia, lapempha boma, ku bungwe lotolera misonkho la MRA, kuti lichotse msonkho wapa malipiro a azibusa a mpingowu. Iwo ati ndi abusa a mpingo okhawu mu CCAP omwe amalipira msonkho wa PAYE pomwe anzizawo mu ma synod a Blantyre ndi Nkhoma satelo ayi. […]
The post Livingstonia Synod ipempha boma kuti lichose msonkho wapamalipiro a azibusa awo appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.