Lero limenelo? – Amalawi afunsa  Mtambo

Zomwe yachita nduna yakale ya boma la m’gwirizano wa Tonse a Timothy Mtambo podzudzula boma pa mavuto omwe akuta dziko lino zadzidzimutsa akatswiri komanso anthu m’dziko lino. Pothilira ndemanga pa zomwe a Mtambo anena dzulo  pa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Lilongwe pomwe anati utsogoleri wa pulezident Chakwera walephera  kuthetsa mavuto omwe a Malawi […]

The post Lero limenelo? – Amalawi afunsa  Mtambo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください