Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati aliyense amene akuchita zozunza anzake m’dziko muno lamulo ligwire ntchito pa iye. Chakwera wayankhula izi pa mwambo wokhazikitsanso kampeni yothana ndi matenda a Cholera komanso Covid-19 ndinso matenda a nkhasa ya khomo la chiberekero omwe mchingerezi atchedwa Human Papilloma Vaccine (HPV) pa bwalo la Madimba m’boma la Likoma. […]
The post Lamulo ligwire ntchito pa aliyense posatengera kuti ndi ndani – Chakwera appeared first on Malawi 24.