Kuli mfuwu ochuluka ku sukulu ya Ukachenjede ya Malawi pomwe bungwe lobwereketsa ngongole kwa ophunzira a m’ma sukulu a Ukachenjede alamura ena mwa ophunzira kumeneku kuti abwenze ma K175 000 omwe analowa kawiri. Sabata yatha, kudali kuvina, kumwa, kumwemwetera pomwe ophunzirawa adalandira K350 000 yomwe ndi ya chaka m’malo mwa K175 000 ya semisita imodzi. […]
The post Kwavuta ku University of Malawi appeared first on Malawi 24.