Kwavuta ku South Bend ku Amereka: Lulu akumusunga ngati nkhuku

…akushopa pa kaunjika wa kumeneko Kumudzi kuno Lulu ndi namandwa oyimba. Zithunzi zake za makabudula pamene ali ku Amereka zikuoneka za mtengo wa patali. Koma oyimba Jolly Bro kapena kuti JB ati tisatengeke nazo. Ku Amereka, akutero ndi JB, Lulu akungomusunga ngati chiweto ku mpanyira wa kumeneko. Ndiponso ati olo kokashopa ndiye ndi ku kaunjika […]

The post Kwavuta ku South Bend ku Amereka: Lulu akumusunga ngati nkhuku appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください