Kwavuta ku Balaka! Nzika zakangalama kuti sizichoka pa ofesi ya Escom mpaka akonze transformer

Nzika zokhudzidwa ndikuvuta kwa magetsi mdera la Majiga 2 mtawuni ya Balaka zayamba mbindikiro pa ofesi za ESCOM pofuna kukakamiza bungweli kuti liwakonzere transformer imene idaonongeka. Sabata yatha, gululi linapeleka kalata ya madandaulo awo ku ofesi ya bungweli kuti ipeleke mayankho ku nkhawa zawo. M’modzi mwa anthuwa, a Pretorius Halidi wati kuzima kwa magetsi kwa […]

The post Kwavuta ku Balaka! Nzika zakangalama kuti sizichoka pa ofesi ya Escom mpaka akonze transformer appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください