Kwanunkha ku Joni: A Malawi enanso 250 achokochedwako, afika mawa mdziko muno

A Malawi okwana 210 omwe athamangitsidwa m’dziko la South Africa akuyembekezereka kufika m’dziko muno mawa. Anthuwa akwanitsa chiwerengero cha anthu omwe athamangitsidwa m’dzikolo mwezi uno kufika pa 490 Kamba koti nzika zina zokwana 280 zinafika m’dziko muno kudzera pa chipata cha boma la Mwanza, sabata yatha.   M’neneri wa nthambi yoona za anthu olowa ndi […]

The post Kwanunkha ku Joni: A Malawi enanso 250 achokochedwako, afika mawa mdziko muno appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください