Anthu m’dziko muno akuyenera kuvala dzilimbe kamba koti pali chiopsezo choti katundu wambiri atha kukwera mitengo kutsatira kuchepa mphamvu kwa ndalama ya kwacha ya dziko lino kuyelekeza ndi ndalama ya dollar ya ku America. Lachinayi sabata ino banki yaikuluyi ya Reserve yalengeza kuti ndalama yakwacha yachepa mphanvu kuyambira lero pa 1 September, 2023. Malingana ndi […]
The post Kwacha yagwa mphamvu appeared first on Malawi24.