Kwacha yada

Kwacha aithyola kholingo, aikang’antha, aichotsa chimbenene, aikong’ontha, aichosa mphamvu. Banki yaikulu ya Reserve yanena lero kuti yachepetsa mphamvu ndalama ya Kwacha ndi ma pelesenti 25. Izi zikutanthauza kuti wani dollar ya ku America yomwe lero ikumafanana mphamvu ndi K825 ya Malawi, kuyambira mawa pa 27 May izifanana mphamvu ndi K1,031 ya ku Malawi. Malingana ndi […]

The post Kwacha yada appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です