Kwabuka kusamvana pakati pa anamwino ndi azamba pomwe mamembala a bungwe la National Organization of Nurses and Midwives of Malawi (NONM) akonza zokatseka ofesi ya bungweli ku Lilongwe pomwe akuloza chala atsogoleri a bungweli polepheletsa zionetsero zomwe zimayenera kukhalako lero iwo osawafotokozera bwino. Nkhaniyi ikubwera pomwe sabata yatha, bungwe la NONM mogwirizana ndi bungwe la […]
The post Kwabuka kusamvana ku NONM pa zionetsero appeared first on Malawi 24.