Kwabhebha ndi ku Illusionz kukubwera Dj Maphorisa; mitengo yafika mpaka K850,000

Inde oyimba Wikise anati K10 sauzande sungamange nyumba, komatu K850 sauzande ndiyambiri zedi: a Malawi mukuitanidwa kukaipatsa moto, kukapinda ziwuno, kudikura ndi Dj Mapholisa, komatu mulimbe mthumba, kuli vimitengo anga ukugula puloti. Lachisanu pa 20 October chaka chino, kuli kutsekulira malo ochitira zisangalaro a Illusionz omwe akupezekera ku Golden Peacock Complex mumzinda wa Lilongwe. Ngati […]

The post Kwabhebha ndi ku Illusionz kukubwera Dj Maphorisa; mitengo yafika mpaka K850,000 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください