Anthu omwe akhudzidwa ndi kusefukila kwa madzi ku Nkope m’boma la Mangochi ati miyoyo yawo ili pa chiopsezo chodwala matenda otsekula mmimba ngakhale kufa ndi njala kumene. Anthu-wa omwe akukhala ku misasa ati nyumba zawo, zimbuzi, chakudya mwa zina zinaonongeka ndipo akusowekera thandizo la msangasanga. Iwo ati akumwa madzi osatetezeka komanso anthu akumangozithandiza paliponse kaamba […]
The post Kwa Nkope ku Mangochi kuli chiopsezo cha matenda otsegula mimba appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.