“Kuthanakuthana pa ndale” – Ken Msonda waopsyeza DPP kuti imuva kunyung’unya

A Ken Msonda omwe ndi m’modzi mwa mamulumuzana omwe awonetsedwa nsana wa njira mchipani cha DPP, akuti chipanichi chaputa mavu nkhomora ndipo waopsyeza kuti chipanichi chiyembekezere kukha madzi ponena kuti pakadali pano wakufa pa ndale sanadziwe, akuti adzimenyera nkhondo mwa mtima bii. A Msonda ayankhula izi kudzera mu kilipi ina yomwe anthu akugawana m’masamba a […]

The post “Kuthanakuthana pa ndale” – Ken Msonda waopsyeza DPP kuti imuva kunyung’unya appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください