Kusowa kwa Shuga kwafika povuta mu mzinda wa Zomba

…Ena adandaula kuti bizinesi yawo yophika kachasu yaima Anthu ochuluka adasonkhana mu shopu ya Chipiku Plus mu mzinda wa Zomba kukanganirana kugula shuga ndipo anthu amakhala maola atatu kapena anayi ali pa mzere asadagule. Malawi24 idayankhula ndi Mai Bridget Vinti omwe adali nawo panzere wogula shugayo ndipo anadandaula kuti akulu akulu a Chipiku Plus akuwalola […]

The post Kusowa kwa Shuga kwafika povuta mu mzinda wa Zomba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください