Kusowa kwa mafuta kwakhudzanso boma la Salima

Kusowa kwa mafuta agalimoto kwakhudza nkhani ya mayendedwe m’boma la Salima pamene mitengo yokwerela magalimoto yakwera. “Kuchoka pa Kamuzu Road kupita pa Golomoti tsopano ndi K5,000 kuyerekeza ndipamene mafuta akakhala kuti akupezeka timachita K3,500,” M’modzi mwawoyendetsa magalimoto pa Kamuzu Road anayankhulana ndi Malawi24 m’mawa uno. Nawo ochita malonda m’bomali omwe amadalira maulendo apa msewu ati […]

The post Kusowa kwa mafuta kwakhudzanso boma la Salima appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください