Kusagwirizana kubuka ku QMAM pamene amwenya akudzudzulidwa kuti akubweretsa chisokonezo

Kusagwirizana kwabuka pakati pa otsatira chipembedzo chachisilamu cha Qadria pamene opembedza akuda akudzudzula opembedza anzawo achimwenye kuti akuwaponderezedwa komanso akuwazunza. Mwazina, opembedza akudawa akuti amwenye akulowerera mzochitika za bungwe la Qadria Muslima Association of Malawi (QMAM) ndi cholinga chobweretsa kugawanikana pakati pa otsatira chipembedzochi. Malingana ndi zomwe Shehe Mhuyudeen watiuza kudzera mu mau omwe wajambula […]

The post Kusagwirizana kubuka ku QMAM pamene amwenya akudzudzulidwa kuti akubweretsa chisokonezo appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください