Kupweteka kwa Thandi Galeta kunatisokoneza, watero mphunzitsi wa Malawi

Mphunzitsi wa timu ya mpira wa manja ya Malawi Sam Kanyenda wati kupweteka kwa Thandi Galeta kunasokoneza timuyi lero pa masewera ake ndi Uganda. Uganda yasambwadza Malawi ndi zigoli 57 kwa 46 lero masanawa mu chikho cha dziko lonse lapansi cha Netball World Cup ku South Africa. Poyankhula mpirawu utatha, Kanyenda anati Malawi zayivuta lero […]

The post Kupweteka kwa Thandi Galeta kunatisokoneza, watero mphunzitsi wa Malawi appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください