…premium yafika pa K79,000 pa mwezi Pomwe mavuto a za chuma afika posauzana, a Malawi omwe amakonda zowonerawonera, alimbe mthumba kaamba koti kampani ya Multichoice Malawi yalengezaso za kukwera mitengo ya ma pakeji a DStv. Lachisanu pa 21 July, 2023 kampaniyi kudzera pa masamba ake anchezo, yalengeza kuti kuyambira pa 1 August chaka chino, mitengo […]
The post Kupsa pansi ndi pamwamba ngati chigumu; Multichoice yakweza mitengo ya DStv appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 
