Kupha nsomba mosatsata malamulo kukuchulukira mnyanja ya Chirwa

Mchitidwe okupha nsomba mosatsata malamulo ukuchulukira mnyanja ya Chilwa chifukwa cha kuchuluka kwa chiwerengero cha anthu amene amakhala mozungulira nyanjayi. Mkulu oyang’anira kaphedwe ka msomba m’boma la Zomba, Elliot Lungu wati kuchuluka kwa anthu kukukolezera mchitidwe okupha msomba mwachisawawa. Mau ake, Lungu wapempha mabungwe ndi anthu okhala mozungulira nyanja ya Chilwa kuti atenge gawo kuteteza […]

The post Kupha nsomba mosatsata malamulo kukuchulukira mnyanja ya Chirwa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください