Gulu la anthu ena omwe akuzitchula kuti nzika zokhudzidwa, zati sizoyenera kuti dziko lino liziloleza maukwati amuna kapena akazi okhaokha. Poyankhula ndi tsamba lino, mmodzi mwa mzika zokhudzidwazi a Edward Kambanje omwe ndi wa chiwiri kwa wapampando wa gululi, ati mchitidwe wa mathanyula ndi mwikho ku dziko lino. A Kambanje anati dziko lili lonse limakhala […]
The post Kuno mathanyula ayi, zatelo nzika zokhudzidwa appeared first on Malawi24.