Ngati sanapiteko ndi komwe ndiye nyimbo ya Buffalo Soldier ya a Gidess Chalamanda asiya kumvera. Koma ngati anapondako kale ati asazabwelerekonso. Dziko la United States of America lalengeza kuti ena mwa adindo a dziko lino asadzapitekonso ati kamba ali ndi chifungo cha katangale. Izi zili mu kalata imene dzikoli latulutsa lero. Malinga ndi kalatayi, amene […]
The post Kuno ayi ti anthu ta katangale inu – dziko la USA lauza a Matemba ndi ena kuti asazapitenso ku Amereka appeared first on Malawi 24.