Ma bishopu a mpingo wa Katolika pansi pa bungwe lawo la Episcopal Conference of Malawi (ECM), ati zomwe wanena mtsogoleri wa mpingowu papa Francis sizikutanthauza kuti mpingowu waloleza maukwati a amuna kapena akazi okhaokha ndipo anenetsa kuti palibe wansembe amene aloledwe kudalitsa maukwati oterewa kuno ku Malawi. Izi zikudza kutsatira nkhani yomwe yadziwika lachiwiri pa […]
The post Kuno ayi – ansembe Akatolika aletsedwa kudalitsa maukwati a amuna kapena akazi okhaokha appeared first on Malawi 24.