‘Kulira kwake ndiye nkumatani abale?’ Chipani cha UTM chalira kumwalira kwa Lucius Banda

Chipani cha UTM chati imfa ya Soldier Lucius Banda mnjowawa kwambiri maka pomwe chipanichi chikulirabe mtsogoleri wawo a Saulos Chilima. Lucius Banda anali mkulu okopa (Campaign Director) anthu mchipani cha UTM. Mneneri wa UTM a Felix Njawala wati ngati chipani sakudziwa kuti nkumatanino ndi momwe imfa yatengera akuluakulu ake motsogozana. Afotokoza a Njawala: “Pomwe a […]

The post ‘Kulira kwake ndiye nkumatani abale?’ Chipani cha UTM chalira kumwalira kwa Lucius Banda appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください