Dzulo lachiwiri tinasiyira poti khothi ku Lilongwe lakana kupeleka chiletso kwa Grezelder Jeffrey chomwe mwa zina chimafuna kuletsa mbali ya mtsogoleri wa chipanichi a Peter Mutharika kuchititsa msonkhano wa akuluakulu a chipani (NGC), ndipo titha kutsimikiza kuti msonkhanowu ulipo ku Mangochi lero, tiyeni tiyembekeze zambiri. Akuluakulu a chipani cholamula chakalechi lero akhamukira ku hotela ya […]
The post Kulinji ku DPP lero? Nsonkhano wa NGC appeared first on Malawi 24.