Nthambi yowona zanyengo yatsutsa mphekesera zomwe zimamveka kuti anthu ena amatha kulenga mphenzi m’matsenga ndipo ena amagula pa mtengo wa 30 kapena 50 kwacha kuti aphe anzawo mwamatsenga. Izi zadziwika pamene nthambiyo inali ndi nkumano ndi atolankhani olemba nkhani za nyengo kuchokera muzigawo komanso mawailesi ndi kanema owulusa mau osiyanasiyana omwe unachitikira ku Liwonde m’boma […]
The post Kulibe mphenzi yogulitsa – atero azanyengo appeared first on Malawi 24.