Anthu okondana chakumwa choyankhulitsa chizungu chija akuyenera kuyamba kulingalira zosiya kumwa chakumwachi ndikuyamba kumwa fanta osaboola mthumba kamba koti kampani yofulula mowa ya Castel yakweza mitengo ya mowa omwe imapanga kuphatikizapo ‘baby gin’. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe kampani ya Castel Malawi Limited yatulutsa lachinayi pa 30 December, 2023 chomwe chikusonyeza mitengo ya tsopano […]
The post Kulibe kothawira, mowa wakwera mtengo appeared first on Malawi 24.