Kukhala mvula ya mphamvu sabata ino – yatelo MET

Unduna wa zachilengedwe ndi kusintha kwa nyengo mogwirizana ndi nthambi yowona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo, ati sabata ino madera ambiri m’dziko muno kugwa mvula ya mphamvu ndipo akuti pali chiopsezo cha madzi osefukira m’madera ena. Izi zili mu kalata yomwe nthambiyi yatulutsa Lamulungu pa 25 February, 2024 yomwe ikufotokoza momwe nyengo msabatayi ikhalire kuyambira […]

The post Kukhala mvula ya mphamvu sabata ino – yatelo MET appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください