Chinkulirano chabuka m’masamba a mchezo pomwe anthu ochuluka akutsutsana za nyimbo yatsopano ya namandwa pamaimbidwe Patience Namadingo ya ‘Affidavit’. Podziwa kuti lonjezo lidadulitsa mutu wa Yohane, Namadingo monga wakhala akulonjezera mmbuyo mosemu lachisanu pa 3 Malitchi, watulutsa nyimbo yatsopano yomwe akuyitchula kuti Affidavit yomweso ndiyoyamba kutulutsa mchaka chino cha 2023. Kanema wa nyimboyi yemwe wathyakulidwa […]
The post Kombola kapena bomba? Nyimbo ya Namadingo yautsa mapili pachigwa appeared first on Malawi24.