Kodi munthu nkukhala yekha? Driemo wazula wake pa Zambia

Ba neba kumatipatsa ulemu ndife amuna anu: Oyimba yemwe watekesa pa Malawi Driemo, watutumutsa gulu pomwe zikumveka kuti wazula wake pa Zambia. Nkhaniyi yadziwika lachinayi pa 24 August pomwe oyimbayu yemwe watenga chikoka cha anthu ochuluka m’dziko muno komaso mayiko ozungulira makamaka azimai, anaika zithuzi za mkazi oganizilidwayu pa tsamba la nchezo. Driemo anaika zithuzi […]

The post Kodi munthu nkukhala yekha? Driemo wazula wake pa Zambia appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください