Bwalo la High Court loona za milandu ya ndalama likuyembekezeka kupereka chigamulo chake ku Lilongwe 2 koloko masanawa pa mulandu wakatangale omwe akuyankha wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Saulos Chilima. Chigamulochi chikhala chopereka chitsogolo ngati kuli koyenera kuti nthambi ya chitetezo ya MDF ipereke zikalata za maumboni ku bwaloli molingana ndi pempho la Chilima […]
The post Khoti lipereka chigamulo kwa a Chilima lero appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.