Khoti lichosa mulandu umodzi pa milandu iwiri yomwe akuzenga a Dalitso Kabambe: Akuti boma lilibe umboni

Bwalo lalikulu la milandu ku Lilongwe lathetsa umodzi mwa milandu yomwe mkulu wakale wa banki ya Reserve a Dalitso Kabambe ndi wachiwiri wao a Henry Mathanga akhala akuyankha okhudza kuganiziridwa kuti ankanamiza bungwe lopereka ngongole la International Monetary Fund. Malingana ndi chigamulo chomwe apereka oweruza a Redson Kapindu, mulandu omwe wathetsedwa ndi oti awiriwa anagwiritsa […]

The post Khoti lichosa mulandu umodzi pa milandu iwiri yomwe akuzenga a Dalitso Kabambe: Akuti boma lilibe umboni appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください