Khoti lati ligamura Mlandu wa Kalindo mawa

Yemwe akumva Mlandu wa Bon Kalindo, Rodrick Michongwe, wati apereka chigamulo chake pa mlanduwu mawa nthawi ya 9 koloko m’mawa. Oyimira a Kalindo pa mlanduwu a Khwima Mchizi anapempha bwaloli kuti a Kalindo apatsidwe belo koma oyimira mbali ya boma anati sikoyenera kutero powopa kuti a Kalindo atha kusokoneza ma umboni a mlandu wawo. A […]

The post Khoti lati ligamura Mlandu wa Kalindo mawa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください