Khonsolo ya mzinda wa Zomba yalimbikitsa anthu okhala mu mzindawu kuti adzichita masewero olimbitsa thupi popeza amathandiza kuti thupi lidzikhala la mphamvu komanso losadwaladwala. Wofalitsa nkhani ku Khonsolo ya mzindawu Sylvia Thawani ndiyemwe wayankhula izi ku Gymkhana Club pomwe khonsoloyi idachititsa masewero olimbitsa thupi (aerobics) komanso mpira wamiyendo ndi wamanja mogwirizana ndi a silikari ankhondo […]
The post Khonsolo ya mzinda wa Zomba yalimbikitsa anthu kuchita masewero olimbitsa thupi appeared first on Malawi 24.