Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe yati itseka miseu ina mzindawu

Pamene ntchito yokonza miseu ina ya mzinda wa Lilongwe idakapitilira, Khonsolo ya mzindawu yati ikhala ikutseka miseu ina monga wa CH 2+ 950 kukafika 2+980 (pafupi ndi Galaxy shop) kuyambila Lolemba pa 25 March, 2024 mpaka Lachisanu pa 6 April, 2024. Malingana ndi chikalata chomwe wasainila ndi Bwanankubwa wa khonsoloyi, Dr McCloud Kam’manja, onse ochita […]

The post Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe yati itseka miseu ina mzindawu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください