Khonsolo ya Lilongwe igwiritsa K2.5 miliyoni kusamutsa pholo la mbendera

Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe yati igwiritsa ntchito ndalama yokwana K2.5 miliyoni ya misonkho ya a Malawi pa ntchito yozula pholo la mbendera ndikukaliyika pa malo ena ku ma ofesi kwawo komweko. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe tsamba lino lawona chomwe chikuzungulira mmasamba a nchezo chomwe chikufotokoza mmene ndalama zigwilitsidwile pa ntchito yonseyi. Chikalatachi […]

The post Khonsolo ya Lilongwe igwiritsa K2.5 miliyoni kusamutsa pholo la mbendera appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください