Khonsolo ya Lilongwe ailetsa kutchetcha chimanga

Boma lauza khonsolo ya mzinda wa Lilongwe (LCC) kuti lisiye kutchetcha chimanga chomwe chinalimidwa mu madera ena a mzinda wa Lilongwe. Khonsolo ya Lilongwe dzulo yakhala ikutchetcha chimanga mu m’madera a Area 43 ndi 11 ponena kuti malamulo salola anthu kulima pa mapuloti kapena m’mbali mwa nsewu mu mzindawu. M’modzi mwa akuluakulu oyang’anira zinthu zosiyanasiyana […]

The post Khonsolo ya Lilongwe ailetsa kutchetcha chimanga appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください