Khonsolo ya Blantyre yaletsa malonda a Chimanga chachiwisi

Wolemba: Gracious Zinazi Khonsolo ya mzinda wa Blantyre yaletsa malonda a chimanga chootcha, chophika ngakhalenso chachiwisi. Izi ndi malinga ndi chikalata chomwe watulutsa kudzera wake Dr Alfred W.D Chanza. Khonsoloyi yanenetsa kuti onse ochita malonda a chimanga chachiwisi akuyenera kutsatira chiletsochi ndipo ngati satero, azatengeredwa ku bwalo la milandu chifukwa uku ndikuphwanya malamulo oyendetsera mzindawu. […]

The post Khonsolo ya Blantyre yaletsa malonda a Chimanga chachiwisi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です