Khonsolo ya Balaka itsutsa zoti yatseka sukulu chifukwa cha njala

Khonsolo ya Balaka yatsutsa mphekesera zomwe zakhala zikuzungulira m’masamba a mchezo osiyanasiyana apa makina a intaneti onena kuti boma latseka sukulu ya pulaimale ya Naliswe yomwe ili m’bomali kamba ka njala yomwe akuti yafika posauzana mdelari. Malingana ndi mneneri wa khonsolo ya Balaka, Mary Makhiringa, maphunziro pa sukuluyi akupitilira monga mwa nthawi zonse ndipo zomwe […]

The post Khonsolo ya Balaka itsutsa zoti yatseka sukulu chifukwa cha njala appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください