Khilisimisi ivutilapo chaka chino, fanta wakwera mtengo

Anthu omwe akuyembekeza kukhala ndi miyambo ngati ukwati ndi ina yomwe zakumwa zozizilitsa kukhosi zimafunika, alimbe mthumba chifukwa fanta, Coca-cola ndi azinzake akwera mtengo, ndipo nkhawa yagwira ana kuti mwina chaka chino khilisimisi itha kulepheleka chifukwa nde kwawilira. Kampani ya Coca-Cola Beverages Malawi yomwe imapanga zakumwa zozizilitsa kukhosi  yalengeza kuti yakweza mitengo yazakumwa zake zonse. […]

The post Khilisimisi ivutilapo chaka chino, fanta wakwera mtengo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください