Khansala wa Ntiya Ward mu mzinda wa Zomba amulumbiritsa

Khansala Maxwell Finiyasi wa Ntiya Ward mu mzinda wa Zomba tsopano amulumbiritsa pankumano wa khonsolo yonse omwe udachitika Lolemba. Mlembi wa ku High Court ku Zomba Hellen Kachala ndiyemwe walumburitsa Khansala Maxwell Finiyasi. Khansala Finiyasi yemwe ndi wachipani cha DPP adapambana pachisankho chachibweredza chomwe chidachitika pa 26 September mwezi watha potsatira imfa ya Khansala Ramsey […]

The post Khansala wa Ntiya Ward mu mzinda wa Zomba amulumbiritsa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください