Khansala Rams Kajosolo wa Mtiya Ward mu Mzinda wa Zomba wamwalira

Khansala wamdera la Mtiya Ward mu Khonsolo ya Mzinda wa Zomba yemwe adali wachipani cha People’s Party (PP) Rams Kajosolo wamwalira pachipatala chachikulu cha Zomba m’bandakucha wa tsiku lachitatu atadwala matenda akuthamanga kwa magazi. Wofalitsa nkhani za Khonsolo ya Mzinda wa Zomba Sylvia Thawani watsimikiza zankhaniyi ndipo wauza Malawi24 kuti Khansala Kajosolo wamwalira atadwala nthawi […]

The post Khansala Rams Kajosolo wa Mtiya Ward mu Mzinda wa Zomba wamwalira appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください