Nkhani yomwe ili mkamwamkamwa pa masamba a nchezo pakadali pano ndi ya osewera ku tsogolo mutimu ya dziko lino, Gabadinho Mhango yemwe lero watutumutsa anthu pomwe akuoneka kuti sanasangalatsidwe kuti anatulutsidwa m’masewero lero. Gaba yemwe pano akusewera ku timu ya Moroka Swallows mdziko la South Africa, anali nawo mgulu la osewera omwe mphunzitsi wa timu […]
The post Khalidwe ndi chuma: Gaba wanyanyula a Malawi appeared first on Malawi 24.