Nduna yoona za malimidwe a Sam Kawale yapempha anthu m’dziko lino kuti ayambe kupanga ulimi wamthilira pofuna kupewa njala pomwe ng’amba yafika posauzana mdziko muno. A Kawale amayankhula izi pomwe amakhazikitsa ntchito yogawa ufa ku maanja omwe akhudzika ndi njala kwa Msakambewa m’boma la Dowa. Iwo ati boma layika ndalama zambiri ku unduna wa za […]
The post Kawale apempha a Malawi kuti alimbikire ulimi wothirira chifukwa ng’amba yafikapo appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.