Poona kuti ophunzira ambili mdziko muno akulephera kupeza nawo mwayi ochita maphunziro msukulu za ukachenjede m’dziko lino kaamba ka chingerezi (English), yemwe ndi katswiri pankhani za maphunziro wapempha boma kuti lichotse chingerezi ngati phunziro limodzi lomuyenereza munthu kuti akachite maphunziro awukachenjede. Katswiriyu yemwe dzina lake ndi a Ben Navitcha anati pali ophunzira ena amachita bwino […]
The post Katswiri pazamaphunziro wati phunziro la chingerezi lisamalepheretse ophunzira kupita ku yunivesite appeared first on Malawi 24.