Katswiri pa nkhani za ndale m’dziko muno a Lyford Chadza, walangiza Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ponena kuti uthenga wake wa SONA ukhale opereka chiyembekezo poona nyenyo zomwe dziko lino likudutsamo. Katswiriyu wanena izi pamene mtsogoleri wa dziko linoyu lero akhala akutsekulira mkumano wa aphungu anyumba ya malamulo lero pa 9 February. Malingana […]
The post Katswiri pandale wati Chakwera asalonjezenso zochuluka appeared first on Malawi 24.