M’modzi mwa akatswiri pandale m’dziko muno a Lyford Chadza, wati mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika akuyenera kusamala pamene mtsogoleriyu wati ali ndi mau opita kwa mtsogoleri wa dziko a Lazarus Chakwera. Katswiriyu wapempha a Mutharika kuti zomwe ayankhule zikhale zobweretsa umodzi pozindikila kuti zomwe iwo angayankhule zili ndi kuthekera kobweretsa umodzi kapena […]
The post Katswiri pandale wati a Mutharika ayankhule zolimbikitsa umodzi appeared first on Malawi 24.