M’modzi mwa akatswiri pa nkhani za ulimi a Leonard Chimwanza, wati zotsatira zomwe unduna wa za ulimi watulutsa ponena kuti dziko lino likolola chakudya chochuluka ndizodzetsa mafunso kutengera ndi momwe mbewu ziliri m’minda yambiri mdziko muno. Malingana ndi a Chimwanza, pakadali pano aliyense akutha kudzionera yekha momwe mbewu zaumira m’minda yochuluka kaamba kavuto lang’amba. Iwo […]
The post Katswiri pa ulimi wati zoti dziko lino likolora chakudya chochuluka zikupereka mafunso appeared first on Malawi 24.